Nehemiah 11:30 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zanowa, Adulamu ndi midzi yake. Ankakhalanso ku Lakisi ndi ku minda yake, ku Azeka ndi midzi yake. Motero ankakhala m'midzi yonse kuyambira ku Beereseba mpaka ku chigwa cha Hinomu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Zanowa, Adulamu ndi midzi yao, Lakisi ndi minda yake, Azeka ndi milaga yake. Ndipo anamanga misasa kuyambira ku Beereseba mpaka chigwa cha Hinomu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zanowa, Adulamu ndi midzi yake, ku Lakisi ndi minda yake, ku Beeriseba mpaka ku chigwa cha Hinomu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Zanowa, Adulamu ndi midzi yao, Lakisi ndi minda yace, Azeka ndi miraga yace. Ndipo anamanga misasa kuyambira ku Beereseba mpaka cigwa ca Hinomu.