Nehemiah 11:31 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu a fuko la Benjamini nawonso adakhala kuyambira ku Geba, kubzola mpaka ku Mikimasi, Aiya, Betele ndi midzi yake,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ana a Benjamini omwe, kuyambira ku Geba pa Mikimasi, ndi Aya, ndi pa Betele ndi milaga yake,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nazonso zidzukulu za Benjamini zinkakhala mʼdera lawo kuyambira ku Geba mpaka ku Mikimasi, Ayiya, Beteli ndi midzi yake,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ana a Benjamini omwe, kuyambira ku Geba pa Mikimasi, ndi Aiya, ndi pa Beteli ndi miraga yace,