Nehemiah 11:36 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Magulu ena a Alevi amene ankakhala m'dziko la Yuda adasamukira ku dziko la Benjamini.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi magawo a Levi anakhala ena ku Yuda, ndi ena ku Benjamini.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Magulu ena a Alevi a ku Yuda ankakhala ku Benjamini.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi magawo a Levi anakhala ena ku Yuda, ndi ena ku Benjamini.