Nehemiah 11:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yowele, mwana wa Zikiri, ndiye amene anali kapitao wao. Ndipo Yuda mwana wa Hasenuwa anali kapitao wachiŵiri wa mumzindamo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi Yowele mwana wa Zikiri ndiye woyang'anira wao, ndi Yuda mwana wa Hasenuwa ndiye wothandizana naye, poyang'anira mudzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yoweli mwana wa Zikiri ndiye anali mtsogoleri wawo, ndipo Yuda mwana wa Hasenuya ndiye amayangʼanira chigawo cha chiwiri cha mzinda.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi Yoeli mwana wa Zikiri ndiye woyang'anira wao, ndi Yuda mwana wa Hasenuwa ndiye wothandizana naye, poyang'anira mudzi.