Nehemiah 12:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yesuwa adabereka Yoyakimu, Yoyakimu adabereka Eliyasibu, Eliyasibu adabereka Yoyada,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi Yesuwa anabala Yoyakimu, ndi Yoyakimu anabala Eliyasibu ndi Eliyasibu anabala Yoyada,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yesuwa anabereka Yowakimu, Yowakimu anabereka Eliyasibu, Eliyasibu anabereka Yoyada.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi Yesuwa anabala Yoyakimu, ndi Yoyakimu anabala Eliasibi ndi Eliasibi anabala Yoyada,