Nehemiah 12:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Wa fuko la Abiya anali Zikiri, wa fuko la Miniyamini, wa fuko la Mowadiya anali Pilitai.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
wa Abiya, Zikiri; wa Miniyamini, wa Mowadiya, Pilitai;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
wa fuko la Abiya anali Zikiri; wa fuko la Miniyamini ndi banja la Maadiya anali Pilitayi;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
wa Abiya, Zikiri; wa Minyamini, wa Moadiya, Pilitai;