Nehemiah 12:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Wa fuko la Yoyaribu anali Matenai, wa fuko la Yedaya anali Uzi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi wa Yoyaribu, Matenai; wa Yedaya, Uzi;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
wa fuko la Yowaribu anali Matenayi; wa fuko la Yedaya anali Uzi;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi wa Yoyaribi, Matani; wa Yedaya, Uzi;