Nehemiah 12:23 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adzukulu a Levi, makamaka atsogoleri a mabanja ao, adalembedwa m'buku la Mbiri, mpaka pa nthaŵi ya Yohanani mwana wa Eliyasibu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ana a Levi, akulu a nyumba za makolo, analembedwa m'buku la machitidwe, mpaka masiku a Yohanani mwana wa Eliyasibu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zidzukulu za Levi, makamaka atsogoleri a mabanja awo analembedwa mʼbuku la mbiri mpaka pa nthawi ya Yohanani mwana wa Eliyasibu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ana a Levi, akuru a nyumba za makolo, analembedwa m'buku la macitidwe, mpaka masiku a Yohanana mwana wa Eliasibu.