Nehemiah 12:25 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mataniya, Bakibukiya, Obadiya, Mesulamu, Talimoni ndi Akubu, anali olonda nyumba zosungiramo chuma pa zipata za ku Nyumba ya Mulungu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mataniya, ndi Bakibukiya, Obadiya, Mesulamu, Talimoni, Akubu, ndiwo odikira akulonda pa nyumba za chuma zili kuzipata.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mataniya, Bakibukiya, Obadiya, Mesulamu, Talimoni ndi Akubu anali olonda nyumba zosungiramo chuma pa zipata za ku Nyumba ya Mulungu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mataniya, ndi Bakibukiya, Obadiya, Mesulamu, Talimoni, Akubi, ndiwo odikira akulonda pa nyumba za cuma ziri kuzipata.