Nehemiah 12:28 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono anthu a m'mabanja a Levi oimba nyimbo, adasonkhana pamodzi, kuchokera ku malo onse ozungulira Yerusalemu, ndiponso ku midzi ya Anetofati.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ana a oimbirawo anasonkhana ochokera ku dziko lozungulira Yerusalemu, ndi kumidzi ya Anetofa,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono anthu a mabanja a Alevi oyimba nyimbo aja anasonkhana pamodzi kuchokera ku madera onse ozungulira Yerusalemu ndiponso ku midzi ya Anetofati,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ana a oyimbirawo anasonkhana ocokera ku dziko lozungulira Yerusalemu, ndi ku midzi ya Anetofati,