Nehemiah 12:29 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kudabwera enanso ochokera ku Betegiligala, ku Geba, ndi ku Azimaveti, pakuti oimba nyimbo anali atamanga midzi yao pozungulira Yerusalemu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi ku Betegiligala, ndi ku minda ya Geba ndi Azimaveti; popeza oimbirawo adadzimangira midzi pozungulira Yerusalemu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Beti-Giligala ndi ku madera a ku Geba ndi Azimaveti, pakuti oyimbawo anali atamanga midzi yawo mozungulira Yerusalemu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi ku Betegiligala, ndi ku minda ya Geba ndi Azimaveti; popeza oyimbirawo adadzimangira midzi pozungulira Yerusalemu.