Nehemiah 13:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nditachita zimenezi, Ayuda adayambanso kubwera ndi zopereka za chachikhumi cha tirigu, vinyo ndi mafuta, kuti azipereka ku nyumba zosungira chuma.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi Ayuda onse anabwera nalo limodzilimodzi la magawo khumi a tirigu, ndi vinyo, ndi mafuta, kunyumba za chuma.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pambuyo pake Ayuda anayambanso kubwera ndi zopereka zawo za chakhumi cha tirigu, vinyo ndi mafuta kuti ziperekedwe ku nyumba yosungiramo chuma.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi Ayuda onse anabwera nalo limodzi limodzi la magawo khumi a tirigu, ndi vinyo, ndi mafuta, ku nyumba za cuma.