Nehemiah 13:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Makolo anu adachitanso motero momwemu, ndipo Mulungu wathu adadzetsa chiwonongeko pa ife ndi pa mzinda uno. Koma inu mukufuna kuutsanso mkwiyo wa Chauta pa Aisraele, pamene mukuipitsa tsiku la sabata motere.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Sanatero kodi makolo anu, ndipo Mulungu wathu anatifikitsira ife ndi mudzi uno choipa ichi chonse? Koma inu muonjezera Israele mkwiyo pakuipsa Sabata.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Makolo anu anachita zomwezi ndipo Mulungu wathu anadzetsa mavuto pa ife ndi pa mzinda uwu. Kodi inu mukufuna kuwutsanso mkwiyo wa Mulungu pa Israeli pamene mukudetsa tsiku la Sabata?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Sanatero kodi makolo anu, ndipo Mulungu wathu anatifikitsira ife ndi mudzi uno coipa ici conse? koma inu muonjezera Israyeli mkwiyo pakuipsa Sabata.