Nehemiah 13:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma zimenezi zisanachitike, wansembe Eliyasibu anali atasankhidwa kuti aziyang'anira zipinda zosungira katundu m'Nyumba ya Mulungu. Chifukwa chomvana ndi Tobiya, iyeyo
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chinkana ichi, Eliyasibu wansembe, woikidwa asunge zipinda za nyumba ya Mulungu wathu, anachita chibale ndi Tobiya,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Izi zisanachitike, wansembe Eliyasibu anali atasankhidwa kukhala woyangʼanira zipinda zosungiramo katundu za Nyumba ya Mulungu. Iyeyu ankagwirizana kwambiri ndi Tobiya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cinkana ici, Eliasibu wansembe, woikidwa asunge zipinda za nyumba ya Mulungu wathu, anacita cibale ndi Tobiya,