Nehemiah 13:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamenepo ndidapsa mtima kwambiri, ndipo ndidamtaya kunja katundu yense wa Tobiya amene anali m'chipindamo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ndinaipidwa nacho kwambiri, motero ndinataya kubwalo akatundu onse a m'nyumba ya Tobiya, kuwachotsa m'chipindamo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndinapsa mtima kwambiri ndipo ndinataya kunja katundu yense wa Tobiya amene anali mʼchipindamo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ndinaipidwa naco kwambiri, motero ndinataya kubwalo akatundu onse a m'nyumba ya Tobiya, kuwacotsa m'cipindamo.