Nehemiah 2:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma pamene akuluakulu aja Sanibalati ndi Tobiya ndiponso Gesemu Mwarabu adamva zimenezi, adayamba kutiseka ndi kutinyoza. Adati, “Kodi chimene mukuchitachi nchiyani? Mukuti muukire mfumu kodi?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma Sanibalati Muhoroni, ndi Tobiya kapolo Mwamoniyo, ndi Gesemu Mwarabu, anamva natiseka pwepwete, natipeputsa, nati, Chiyani ichi muchichita? Mulikupandukira mfumu kodi?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Sanibalati wa ku Horoni, Tobiya wa ku Amoni ndi Gesemu Mwarabu atamva zimenezi, anatiseka ndi kutinyoza. Iwo anafunsa kuti, “Kodi muti ndi chiyani chimene mukuchitachi? Kodi mufuna kuwukira mfumu?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma Sanibalati Mhoroni, ndi Tobiya kapolo M-amoniyo, ndi Gesemu M-arabu, anamva natiseka pwepwete, natipeputsa, nati, Ciani ici mucicita? Mulikupandukira mfumu kodi?