Nehemiah 3:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Malakiya, mwana wa Rekabu, wolamulira dera la Betehakeremu, adakonza Chipata cha Zinyalala. Adachimanganso, naikira zitseko zake, zotsekera zake ndi mipiringidzo yake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi Chipata cha Kudzala anachikonza Malikiya mwana wa Rekabu, mkulu wa dziko la Betehakeremu; anachimanga, naika zitseko zake, zokowera zake, ndi mipiringidzo yake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chipata cha Zinyalala chinakonzedwa ndi Malikiya mwana wa Rekabu, wolamulira chigawo cha Beti-Hakeremu. Iye anachimanganso ndi kuyika zitseko zake, zotsekera zake ndi mipiringidzo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi cipata ca kudzala anacikonza Malikiya mwana wa Rekabu, mkuru wa dziko la Bete Hakeremu; anacimanga, naika zitseko zace, zokowera zace, ndi mipiringidzo yace.