Nehemiah 3:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu a ku Yeriko adamanga chigawo china pambalipa, ndipo Zakuri, mwana wa Imuri, adamanga chigawo chinanso kuyandikana ndi chimenechi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi pambali pake anamanga amuna a ku Yeriko. Ndi pambali pao anamanga Zakuri mwana wa Imuri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu a ku Yeriko anamanga chigawo china pambali pake ndipo Zakuri mwana wa Imuri anamanga chigawo chinanso choyandikana nawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi pambali pace anamanga amuna a ku Yeriko. Ndi pambali pao anamanga Zakuri mwana wa Imri.