Nehemiah 3:28 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kuyambira ku Chipata cha Akavalo, ansembe ena ankakonza khoma, aliyense moyang'anana ndi nyumba yake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kumtunda kwa chipata cha akavalo anakonza ansembe, yense pandunji pa nyumba yake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kuyambira ku Chipata cha Akavalo anakonza ndi ansembe ena ndipo aliyense amakonza khoma loyangʼanana ndi nyumba yake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kumtunda kwa cipata ca akavalo anakonza ansembe, yense pandunji pa nyumba yace.