Nehemiah 3:32 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo pakati pa chipinda chapamwamba chapangodya ndi Chipata cha Nkhosa, amisiri a golide ndi anthu amalonda adakonza chigawo chao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi pakati pa chipinda chosanja cha kungodya ndi chipata chankhosa anakonza osula golide ndi ochita malonda.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo pakati pa chipinda chapamwamba chapangodya ndi Chipata cha Nkhosa anakonza ndi amisiri a golide ndi anthu amalonda.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi pakati pa cipinda cosanja ca kungondya ndi cipata cankhosa anakonza osula golidi ndi ocita malonda.