Nehemiah 3:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pambali pa iwowo Meremoti, mwana wa Uriya, mwana wa Hakozi, adakonza chigawo china. Pambali pa iwowo Mesulamu, mwana wa Berekiya, mwana wa Mesezabele, adakonza chigawo china. Pambali pa iwowo Zadoki, mwana wa Baana, adakonza chigawo china.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi pambali pao anakonza Meremoti mwana wa Uriya, mwana wa Hakozi. Ndi pambali pao anakonza Mesulamu mwana wa Berekiya, mwana wa Mesezabele. Ndi pambali pao anakonza Zadoki mwana wa Baana.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Meremoti mwana wa Uriya, mwana wa Hakozi, anakonza chigawo choyandikana nacho. Motsatana naye, Mesulamu mwana wa Berekiya, mwana wa Mesezabeli anakonza chigawo china. Pambali pake, Zadoki mwana wa Baana anakonzanso chigawo china.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi pambali pao anakonza Meremoti mwana wa Uliya, mwana wa Kozi. Ndi pambali pao anakonza Mesulamu mwana wa Berekiya, mwana wa Mesezabele. Ndi pambali pao anakonza Zadoki mwana wa Baana.