Nehemiah 3:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pambali pa iwowo, Melatiya Mgibiyoni ndi Yadoni Mmeronoti, ndiponso anthu a ku Gibiyoni ndi a ku Mizipa, adakonza chigawo chao mpaka ku nyumba ya bwanamkubwa wa chigawo cha Patsidya pa Yufurate.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi pambali pao anakonza Melatiya Mgibeoni, ndi Yadoni Mmeronoti, ndi amuna a ku Gibiyoni, ndi a ku Mizipa, wa ulamuliro wa chiwanga tsidya lino la mtsinje.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pambali pawo Melatiya Mgibeyoni ndi Yadoni Mmerenoti ndiponso anthu a ku Gibiyoni ndi a ku Mizipa anakonza chigawo chawo mpaka ku nyumba ya bwanamkubwa wa chigawo cha Patsidya pa Yufurate.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi pambali pao anakonza Melatiya Mgibeoni, ndi Yadoni Mheronoti, ndi amuna a ku Gibeoni, ndi a ku Mizipa, wa ulamuliro wa ciwanga tsidya lino la mtsinje.