Nehemiah 4:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Ayuda okhala pafupi ndi adani athuwo ankabwera natichenjeza kakhumi konse kuti “Iwo aja adzafika kudzalimbana nanu kuchokera kulikonse kumene amakhala.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kunali, atafika Ayuda okhala pafupi pao ochokera pamalo ponse, anatiuza ife kakhumi, Bwererani kwa ife.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo Ayuda amene ankhala pafupi ndi adani athuwo anabwera kakhumi konse kuchokera konse kumene ankakhala kudzatiwuza kuti tibwereko ku ntchito.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kunali, atafika Ayuda okhala pafupi pao ocokera pamalo ponse, anatiuza ife kakhumi, Bwererani kwa ife.