Nehemiah 4:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu onyamula zinyalala aja ankagwira ntchito ndi dzanja limodzi, kwinaku atagwira chida chankhondo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iwo omanga linga, ndi iwo osenza katundu, posenza, anachita aliyense ndi dzanja lake lina logwira ntchito, ndi lina logwira chida;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
amene ankamanga khoma. Anthu onyamula zinyalala aja ankagwira ntchito ndi dzanja limodzi, dzanja linali atanyamula chida chankhondo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iwo omanga linga, ndi iwo osenza katundu, posenza, anacita ali yense ndi dzanja lace lina logwira nchito, ndi lina logwira cida;