Nehemiah 4:21 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Choncho enafe tinkagwira ntchito, ndipo theka lina la anthuwo linkagwira zida zankhondo, kuyambira m'matandakucha mpaka nyenyezi zitaoneka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Momwemo tinalikugwira ntchito; gawo lina la iwo linagwira nthungo kuyambira mbandakucha mpaka zatuluka nyenyezi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho enafe tinapitiriza kugwira ntchito, pamene theka lina linkanyamula mikondo kuyambira mʼbandakucha mpaka nyenyezi zitaoneka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Momwemo tinalikugwira nchito; gawo lina la iwo linagwira nthungo kuyambira mbanda kuca mpaka zaturuka nyenyezi.