Nehemiah 4:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero tidamangabe khoma, ndipo khoma lonse tidatha kulimanga mpaka theka la msinkhu wake, chifukwa chakuti anthu adaaikapo mtima pa ntchitoyo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma tinamanga lingali, ndi linga lonse linalumikizana kufikira pakatimpakati; popeza mitima ya anthu inalunjika kuntchito.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho ife tinamangabe khomalo kufikira lonse litafika theka la msinkhu wake, chifukwa chakuti anthu anagwira ntchitoyo ndi mtima wawo wonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma tinamanga lingali, ndi linga lonse linalumikizana kufikira pakati mpakati; popeza mitima ya anthu inalunjika kunchito.