Nehemiah 5:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono anthu ena pamodzi ndi akazi ao adayamba kudandaula kwambiri chifukwa cha Ayuda anzao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo panamveka kulira kwakukulu kwa anthu ndi akazi ao kudandaula pa abale ao Ayuda.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono anthu ena ndi akazi awo anayamba kudandaula kwambiri chifukwa cha Ayuda anzawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo panamveka kulira kwakukuru kwa anthu ndi akazi ao kudandaula pa abale ao Ayuda.