Nehemiah 5:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kuti tipeze bwino, kumbukirani, Inu Mulungu wanga, zonse zimene ndidaŵachitira anthuzi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mundikumbukire Mulungu, zindikomere zonse ndinachitira anthu awa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kuti zinthu zindiyendere bwino, kumbukirani Yehova Mulungu wanga pa zonse zimene ndachitira anthu awa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mundikumbukire Mulungu, zindikomere zonse ndinacitira anthu awa.