Nehemiah 5:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pakuti panali ena amene ankati, “Ife ndi ana athu tikuchuluka kwambiri, motero tikusoŵa tirigu wakudya, kuti tikhale ndi moyo.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Popeza panali ena akuti, Ife, ana athu aamuna ndi aakazi, ndife ambiri; talandira tirigu, kuti tidye tikhale ndi moyo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ena ankanena kuti, “Ife ndi ana athu aamuna ndi aakazi, tilipo ochuluka kwambiri. Choncho tikufuna tirigu kuti tidye ndi kukhala ndi moyo.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Popeza panali ena akuti, Ife, ana athu amuna ndi akazi, ndife ambiri; talandira tirigu, kuti tidye tikhale ndi moyo.