Nehemiah 5:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Panalinso ena amene ankati, “Ife tikuchita kupereka minda yathu, mitengo yathu yamphesa, pamodzi ndi nyumba zathu, ngati chikole, kuti tipeze tirigu, poti njala yatipha.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Panali enanso akuti, Tili kupereka chikole minda yathu, ndi minda yathu yampesa ndi nyumba zathu; kuti tilandire tirigu chifukwa cha njalayi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Panali ena amene ankanena kuti, “Ife tikuchita kupereka minda yathu, mitengo yathu ya mphesa ndi nyumba zathu ngati chikole kuti tipeze tirigu chifukwa njala yakula.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Panali enanso akuti, Tirikupereka cikole minda yathu, ndi minda yathu yampesa ndi nyumba zathu; kuti tilandire tirigu cifukwa ca njalayi.