Nehemiah 5:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Panali enanso amene ankati, “Ife tachita kukongola ndalama kuti tikhome msonkho wa minda yathu kwa mfumu, ndiponso kuti tikhomere mitengo yathu yamphesa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Panali enanso akuti, Takongola ndalama za msonkho wa mfumu; taperekapo chikole minda yathu, ndi minda yathu yampesa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Panalinso ena amene ankanena kuti, “ife tinachita kukongola ndalama zoti tipereke msonkho wa minda ndi mitengo yathu ya mphesa kwa mfumu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Panali enanso akuti, Takongola ndarama za msonkho wa mfumu; taperekapo cikole minda yathu, ndi minda yathu yampesa.