Nehemiah 6:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kenaka ndidazindikira kuti Mulungu sadamtume, koma ankandinenera zimenezi chifukwa chakuti Tobiya ndi Sanibalati ndiwo adaamlemba ntchito imeneyi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ndinazindikira kuti sanamtume Mulungu; koma ananena choneneracho pa ine, popeza Tobiya ndi Sanibalati adamlembera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndinazindikira kuti Mulungu sanamutume koma kuti anayankhula mawu oloserawa motsutsana nane chifukwa Tobiya ndi Sanibalati anamulemba ntchitoyi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ndinazindikira kuti sanamtuma Mulungu; koma ananena coneneraco pa ine, popeza Tobiya ndi Sanibalati adamlembera.