Nehemiah 6:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Patapita masiku 52, pa tsiku la 25 la mwezi wa Eluli, khoma lija adatsiriza kumanga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo linga linatsirizika pa tsiku la makumi awiri ndi lachisanu la mwezi wa Eluli, titalimanga masiku makumi asanu mphambu awiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo khoma linatsirizidwa kumanga pa tsiku la 25 la mwezi wa Eluli. Linamangidwa pa masiku okwana 52.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo linga linatsirizika pa tsiku la makumi awiri ndi lacisanu la mwezi wa Eluli, titalimanga masiku makumi asanu mphambu awiri.