Nehemiah 6:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kuwonjezera apo, nthaŵi imeneyo atsogoleri a ku Yuda ankalemberana makalata ndi Tobiya,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Masikuwo aufulu a Yuda analemberanso akalata ambiri kwa Tobiya; ndipo anawafikanso akalata ake a Tobiya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Komanso masiku amenewo anthu olemekezeka a ku Yuda ankalemberana naye makalata ambiri ndi Tobiyayo,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Masikuwo aufulu a Yuda analemberanso akalata ambiri kwa Tobiya; ndipo anawafikanso akalata ace a Tobiya.