Nehemiah 6:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamenepo Sanibalati adatumanso wantchito wake kachisanu kwa ine. Iye anali ndi kalata yosamata m'manja mwake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo Sanibalati anatuma mnyamata wake kwa ine kachisanu, ndi kalata wosatseka m'dzanja mwake;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono kachisanu, Sanibalati anatumiza wantchito wake ndi kalata yosamata.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo Sanibalati anatuma mnyamata wace kwa ine kacisanu, ndi kalata wosatseka m'dzanja mwace;