Nehemiah 7:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Khoma la mzinda lija litamangidwa, ndidaikira zitseko, ndipo alonda a ku Nyumba ya Mulungu, anthu oimba nyimbo ndiponso Alevi adasankhidwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo atatha kumanga linga, ndinaika zitseko, nakhazika odikira, ndi oimbira, ndi Alevi;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Khoma linamangidwa ndipo zitseko zinayikidwa. Pambuyo pake alonda a Nyumba ya Mulungu, oyimba nyimbo ndiponso Alevi anasankhidwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo atatha kumanga linga, ndinaika zitseko, nakhazika odikira, ndi oyimbira, ndi Alevi;