Nehemiah 7:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
A banja la Pahatimowabu, ndiye kuti zidzukulu za Yesuwa ndi Yowabu 2,818.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ana a Pahatimowabu, a ana a Yesuwa ndi Yowabu, zikwi ziwiri mphambu mazana asanu ndi atatu kudza khumi limodzi ndi asanu ndi atatu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zidzukulu za Pahati-Mowabu (kudzera mu mʼbado wa Yesuwa ndi Yowabu) — 2,818
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ana a Pakati Moabu, a ana a Yesuwa ndi Yoabu, zikwi ziwiri mphambu mazana asanu ndi atatu kudza khumi limodzi ndi asanu ndi atatu.