Nehemiah 7:34 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
A banja la Elamu wina 1,254.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ana a Elamu winayo, chikwi chimodzi mphambu mazana awiri ndi makumi asanu kudza anai.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ana a Elamu wina — 1,254
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ana a Elamu winayo, cikwi cimodzi mphambu mazana awiri ndi makumi asanu kudza anai.