Nehemiah 7:44 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Oimba nyimbo anali aŵa: a banja la Asafu 148.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Oimbira: ana a Asafu, zana limodzi mphambu makumi anai kudza asanu ndi atatu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu oyimba: Zidzukulu za Asafu — 148.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Oyimbira: ana a Asafu, zana limodzi mphambu makumi anai kudza asanu ndi atatu.