Nehemiah 7:60 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Antchito onse a ku Nyumba ya Mulungu, kuphatikizapo zidzukulu za antchito a Solomoni, onse pamodzi analipo 392.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anetini onse, ndi ana a akapolo a Solomoni, ndiwo mazana atatu mphambu makumi asanu ndi anai kudza awiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu onse ogwira ntchito ku Nyumba ya Mulungu pamodzi ndi zidzukulu za antchito a Solomoni analipo — 392.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anetini onse, ndi ana a akapolo a Solomo, ndiwo mazana atatu mphambu makumi asanu ndi anai kudza awiri.