Nehemiah 7:69 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ngamira zao zinalipo 435, ndipo abulu ao analipo 6,720.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ngamira zao mazana anai mphambu makumi atatu kudza asanu; abulu ao zikwi zisanu ndi chimodzi mphambu mazana asanu ndi awiri kudza makumi awiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngamira zawo zinalipo 435 ndipo abulu analipo 6,720.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ngamira zao mazana anai mphambu makumi atatu kudza asanu aburu ao zikwi zisanu ndi cimodzi mphambu mazana asanu ndi awiri kudza makumi awiri.