Nehemiah 9:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mudaŵadziŵitsa kuti tsiku lanu la Sabata ndi lopatulika, ndipo mudaŵapatsa malamulo, malangizo, ndiponso mau anu, kudzera mwa Mose mtumiki wanu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi Sabata lanu lopatulika munawadziwitsa, nimunawalamulira malamulo, ndi malemba, ndi chilamulo, mwa dzanja la Mose mtumiki wanu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu munawadziwitsa kuti tsiku lanu la Sabata ndi loyera ndipo munawapatsa malamulo ndi ziphunzitso.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi Sabata lanu lopatulika munawadziwitsa, nimunawalamulira malamulo, ndi malemba, ndi cilamulo, mwa dzanja la Mose mtumiki wanu;