Nehemiah 9:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngakhale pamene adadzipangira fano la mwanawang'ombe, namanena kuti, ‘Uyu ndiye Mulungu wathu amene adatitulutsa ku dziko la Ejipito,’ ndipo ngakhale adachita zinthu zoipitsitsa zokunyozani,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ngakhale apa atadzipangira mwanawang'ombe woyenga, nati, Suyu Mulungu wako anakukweza kuchokera ku Ejipito, nachita zopeputsa zazikulu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngakhale pamene iwo anadziwumbira fano la mwana wangʼombe ndi kuti, ‘Uyu ndi mulungu wanu amene anakutulutsani mʼdziko la Igupto,’ kapena pamene anachita chipongwe choopsa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ngakhale apa atadzipangira mwana wa ng'ombe woyenga, nati, Suyu Mulungu wako anakukweza kucokera ku Aigupto, nacita zopeputsa zazikuru;