Nehemiah 9:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu mudaŵapatsa mzimu wanu wabwino kuti aziŵalangiza. Simudaŵamane chakudya cha mana chija, ndipo mudaŵapatsa madzi akumwa, kuti aphe ludzu lao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Munawapatsanso mzimu wanu wokoma kuwalangiza, ndipo simunawamana mana anu pakamwa pao; munawapatsanso madzi pa ludzu lao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu munawapatsa mzimu wanu wabwino kuti uwalangize. Inu simunawamane chakudya cha mana chija, ndipo munawapatsa madzi akumwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Munawapatsanso mzimu wanu wokoma kuwalangiza, ndipo simunawamana mana anu pakamwa pao; munawapatsanso madzi pa ludzu lao.