Nehemiah 9:23 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mudachulukitsa zidzukulu zao ngati nyenyezi zamumlengalenga. Mudaŵaloŵetsa m'dziko limene mudaauza makolo ao kuti adzalilandira nkukhala lao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ana aonso munawachulukitsa monga nyenyezi za m'mwamba, nimunawalowetsa m'dziko mudalinena kwa makolo ao, alowemo likhale laolao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Munachulukitsa ana awo aamuna ngati nyenyezi za mlengalenga. Ndipo munawabweretsa mʼdziko limene munawuza makolo awo kuti alilowe ndi kulitenga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ana aonso munawacurukitsa monga nyenyezi za m'mwamba, nimunawalowetsa m'dziko mudalinena kwa makolo ao, alowemo likhale lao lao.