Nehemiah 9:31 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngakhale zinali choncho, Inu simudaŵaononge kotheratu, kapena kuŵasiya, pakuti Inu ndinu Mulungu wokoma mtima ndi wachifundo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mwa nsoni zanu zochuluka simunawatha, kapena kuwataya; popeza Inu ndinu Mulungu wa chisomo ndi chifundo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Komabe mwachifundo chanu chachikulu simuwatheretu kapena kuwataya pakuti ndinu Mulungu wokoma mtima ndi wachifundo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mwa nsoni zanu zocuruka simunawatha, kapena kuwataya; popeza Inu ndinu Mulungu wa cisomo ndi cifundo.