Nehemiah 9:33 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Komabe Inu mwakhala olungama pa zonse zimene zatigwera, ndipo mwachita zokhulupirika, koma ife tachita zolakwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma Inu ndinu wolungama mwa zonse zatigwera; pakuti mwachita zoona, koma ife tachita choipa;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Inu mwakhala wolungama pa zonse zimene zakhala zikutichitikira. Mwachita zokhulupirika, koma ife tachita zolakwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma Inu ndinu wolungama mwa zonse zatigwera; pakuti mwacita zoona, koma ife tacita coipa;