Nehemiah 9:36 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Onani, ife ndife akapolo lero lino, ndife akapolo m'dziko limene mudapatsa makolo athu, kuti azidya zipatso zake ndi zabwino zake zonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tapenyani, ife lero ndife akapolo, ndi dzikoli mudalipereka kwa makolo athu kudya zipatso zake ndi zokoma zake, taonani, ife ndife akapolo m'menemo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Tsono, taonani! Ife lero ndife akapolo, ndife akapolo mʼdziko limene munapereka kwa makolo athu kuti azidya zipatso zake ndi zabwino zake zonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tapenyani, ife lero ndife akapolo, ndi dzikoli mudalipereka kwa makolo athu kudya zipatso zace ndi zokoma zace, taonani, ife ndife akapolo m'menemo.