Numbers 1:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono ataŵerenga maina onse a m'fuko la Rubeni, adapezeka kuti ali 46,500.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
owerengedwa ao a fuko la Rubeni, ndiwo zikwi makumi anai mphambu zisanu ndi chimodzi kudza mazana asanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chiwerengero cha anthu ochokera mʼfuko la Rubeni chinali 46,500.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
owerengedwa ao a pfuko la Rubeni, ndiwo zikwi makumi anai mphambu zisanu ndi cimodzi kudza mazana asanu.