Numbers 1:27 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono ataŵerenga maina onse a m'fuko la Yuda, adapezeka kuti ali 74,600.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
owerengedwa ao a fuko la Yuda, ndiwo zikwi makumi asanu ndi awiri mphambu zinai kudza mazana asanu ndi limodzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chiwerengero cha anthu ochokera mʼfuko la Yuda chinali 74, 600.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
owerengedwa ao a pfuko la Yuda, ndiwo zikwi makumi asanu ndi awiri mphambu zinai kudza mazana asanu ndi limodzi.